Nyimbo ya Solomo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mutu wako ndi wokwezeka ngati Karimeli.+ Tsitsi+ la m’mutu mwako lili ngati ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira,+ ndipo mfumu yatengeka nalo tsitsi lako lalitalilo.+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:5 Nsanja ya Olonda,8/15/1996, tsa. 7
5 Mutu wako ndi wokwezeka ngati Karimeli.+ Tsitsi+ la m’mutu mwako lili ngati ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira,+ ndipo mfumu yatengeka nalo tsitsi lako lalitalilo.+