-
Nyimbo ya Solomo 7:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndipo mʼkamwa mwako mununkhire ngati vinyo wabwino kwambiri.”
“Adutse mwamyaa kukhosi kwa wokondedwa wanga,
Ngati vinyo amene amadutsa mwamyaa pakamwa nʼkuyambitsa tulo kwa amuna.
-