Nyimbo ya Solomo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’kamwa mwako mukhale ngati vinyo wabwino kwambiri+ amene amatsetserekera kukhosi kwa wokondedwa wanga mwamyaa,+ amene amayenderera pang’onopang’ono pamilomo ya anthu amene akugona.”
9 M’kamwa mwako mukhale ngati vinyo wabwino kwambiri+ amene amatsetserekera kukhosi kwa wokondedwa wanga mwamyaa,+ amene amayenderera pang’onopang’ono pamilomo ya anthu amene akugona.”