-
Yesaya 3:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Aliyense adzagwira mʼbale wake mʼnyumba mwa bambo ake nʼkumuuza kuti:
“Iwe uli ndi nsalu, ndiye ukhale wolamulira wathu.
Uzilamulira mulu wa bwinjawu.”
-