Yesaya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense adzagwira m’bale wake m’nyumba mwa bambo ake n’kumuuza kuti: “Iwe uli ndi nsalu. Choncho ukhale wolamulira+ wathu ndipo uzilamulira mulu wa bwinjawu.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Yesaya 1, ptsa. 56-57
6 Aliyense adzagwira m’bale wake m’nyumba mwa bambo ake n’kumuuza kuti: “Iwe uli ndi nsalu. Choncho ukhale wolamulira+ wathu ndipo uzilamulira mulu wa bwinjawu.”