Yesaya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imvani mawu a Yehova,+ inu olamulira ankhanza+ a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora. Yesaya 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Olamulira ako onse ankhanza+ athawa nthawi imodzi.+ Atengedwa ukaidi popanda kugwiritsa ntchito uta. Anthu ako onse amene apezeka atengedwa ukaidi limodzi.+ Iwo anali atathawira kutali. Yohane 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yesu atadziwa kuti iwo akufuna kumugwira kuti amuveke ufumu, anachoka+ ndi kupitanso kuphiri yekhayekha.
10 Imvani mawu a Yehova,+ inu olamulira ankhanza+ a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.
3 Olamulira ako onse ankhanza+ athawa nthawi imodzi.+ Atengedwa ukaidi popanda kugwiritsa ntchito uta. Anthu ako onse amene apezeka atengedwa ukaidi limodzi.+ Iwo anali atathawira kutali.
15 Choncho Yesu atadziwa kuti iwo akufuna kumugwira kuti amuveke ufumu, anachoka+ ndi kupitanso kuphiri yekhayekha.