Yesaya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsiku limenelo, chinthu chimene Yehova adzachiphukitse chidzakhala chokongola komanso chaulemerero. Zipatso za mʼdzikolo zidzakhala zonyaditsa ndi zokongola kwa Aisiraeli amene adzapulumuke.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Yesaya 1, ptsa. 62-67
2 Tsiku limenelo, chinthu chimene Yehova adzachiphukitse chidzakhala chokongola komanso chaulemerero. Zipatso za mʼdzikolo zidzakhala zonyaditsa ndi zokongola kwa Aisiraeli amene adzapulumuke.+