Yesaya 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano mʼmasiku a Ahazi+ mwana wa Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya Yuda, Rezini mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anapita kukamenyana ndi anthu amumzinda wa Yerusalemu koma analephera kulanda mzindawo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Yesaya 1, ptsa. 101-102
7 Tsopano mʼmasiku a Ahazi+ mwana wa Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya Yuda, Rezini mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anapita kukamenyana ndi anthu amumzinda wa Yerusalemu koma analephera kulanda mzindawo.+