Yesaya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yesaya ananena kuti: “Tamverani inu a mʼnyumba ya Davide. Kodi zimene mukuchita poyesa kuleza mtima kwa anthu nʼzosakwanira kwa inu? Kodi mukufunanso kuyesa kuleza mtima kwa Mulungu?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:13 Yesaya 1, tsa. 107
13 Kenako Yesaya ananena kuti: “Tamverani inu a mʼnyumba ya Davide. Kodi zimene mukuchita poyesa kuleza mtima kwa anthu nʼzosakwanira kwa inu? Kodi mukufunanso kuyesa kuleza mtima kwa Mulungu?+