Yesaya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero mneneriyo anati: “Tamverani inu a nyumba ya Davide. Kodi mukuona ngati n’zazing’ono kuti muzitopetsa anthu, ndiponso kuti mutopetse Mulungu wanga?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:13 Yesaya 1, tsa. 107
13 Chotero mneneriyo anati: “Tamverani inu a nyumba ya Davide. Kodi mukuona ngati n’zazing’ono kuti muzitopetsa anthu, ndiponso kuti mutopetse Mulungu wanga?+