-
Yesaya 10:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma iye sadzafuna kuchita zimenezi
Ndipo mtima wake sudzakonza zoti achite zimenezi.
Koma chifukwa chakuti mumtima mwake amaganiza zowononga,
Zoti awonongeretu mitundu yambiri, osati yochepa,
-