Yesaya 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale iye atakhala kuti si wotero, adzafunabe kuchita zimenezi. Ngakhale mtima wake utakhala kuti si wotero, adzakonza zoti achite zimenezi, chifukwa chakuti mumtima mwake amaganiza zowononga+ ndiponso zoti awonongeretu mitundu yambiri.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:7 Yesaya 1, tsa. 146
7 Ngakhale iye atakhala kuti si wotero, adzafunabe kuchita zimenezi. Ngakhale mtima wake utakhala kuti si wotero, adzakonza zoti achite zimenezi, chifukwa chakuti mumtima mwake amaganiza zowononga+ ndiponso zoti awonongeretu mitundu yambiri.+