2 Mafumu 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kodi milungu ya Hamati+ ndi Aripadi+ ili kuti? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu,+ Hena,+ ndi Iva?+ Kodi yalanditsa Samariya m’manja mwanga?+ Yesaya 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi milungu+ ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawalanditsa?+ Kodi inalanditsa Gozani,+ Harana,+ Rezefi ndi ana a Edeni+ amene anali ku Tela-sara?
34 Kodi milungu ya Hamati+ ndi Aripadi+ ili kuti? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu,+ Hena,+ ndi Iva?+ Kodi yalanditsa Samariya m’manja mwanga?+
12 Kodi milungu+ ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawalanditsa?+ Kodi inalanditsa Gozani,+ Harana,+ Rezefi ndi ana a Edeni+ amene anali ku Tela-sara?