Maliro 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adani ako onse akukutsegulira pakamwa.+Akuimba mluzu ndi kukukukutira mano.+ Iwo akunena kuti: “Ameneyu timumeza.+Ndithu, lero ndi tsiku limene takhala tikuyembekezera.+ Lafikadi! Taliona!”+ Mika 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Tsopano mitundu yambiri ya anthu idzasonkhana kuti ikuukire. Mitunduyo ikunena kuti, ‘Tiyeni timuwononge ndipo maso athu aone kuwonongeka kwa Ziyoni.’+
16 Adani ako onse akukutsegulira pakamwa.+Akuimba mluzu ndi kukukukutira mano.+ Iwo akunena kuti: “Ameneyu timumeza.+Ndithu, lero ndi tsiku limene takhala tikuyembekezera.+ Lafikadi! Taliona!”+
11 “Tsopano mitundu yambiri ya anthu idzasonkhana kuti ikuukire. Mitunduyo ikunena kuti, ‘Tiyeni timuwononge ndipo maso athu aone kuwonongeka kwa Ziyoni.’+