Yobu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+ Salimo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anditsegulira pakamwa pawo mondiopseza,+Ngati mkango wokhadzula nyama umenenso ukubangula.+ Salimo 35:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amatsegula kwambiri pakamwa pawo kuti atsutsane nane.+Iwo amati: “Eya! Eya! Tadzionera tokha.”+ Salimo 109:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+
10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+
2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+