Yesaya 49:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale kuti panopa malo ako ndi owonongeka, osakazidwa ndiponso abwinja,+ ngakhale kuti panopa malo ako ndi osatakasuka mokwanira kuti n’kukhalamo bwinobwino, ndipo okumeza akhala kutali,+ Yeremiya 51:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Nebukadirezara mfumu ya Babulo wandidya.+ Wandisokoneza ndi kundisandutsa chiwiya chopanda kanthu. Wandimeza ngati chinjoka chachikulu.+ Wakhuta zinthu zanga zokoma ndipo wanditsukuluza.
19 Ngakhale kuti panopa malo ako ndi owonongeka, osakazidwa ndiponso abwinja,+ ngakhale kuti panopa malo ako ndi osatakasuka mokwanira kuti n’kukhalamo bwinobwino, ndipo okumeza akhala kutali,+
34 “Nebukadirezara mfumu ya Babulo wandidya.+ Wandisokoneza ndi kundisandutsa chiwiya chopanda kanthu. Wandimeza ngati chinjoka chachikulu.+ Wakhuta zinthu zanga zokoma ndipo wanditsukuluza.