Yeremiya 51:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndidzalanga Beli+ ku Babulo ndipo ndidzamulavulitsa zimene wameza.+ Mitundu ya anthu sidzakhamukiranso kwa iye.+ Kuwonjezera apo, mpanda wa Babulo udzagwa.+ Maliro 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adani ako onse akukutsegulira pakamwa.+Akuimba mluzu ndi kukukukutira mano.+ Iwo akunena kuti: “Ameneyu timumeza.+Ndithu, lero ndi tsiku limene takhala tikuyembekezera.+ Lafikadi! Taliona!”+
44 Ndidzalanga Beli+ ku Babulo ndipo ndidzamulavulitsa zimene wameza.+ Mitundu ya anthu sidzakhamukiranso kwa iye.+ Kuwonjezera apo, mpanda wa Babulo udzagwa.+
16 Adani ako onse akukutsegulira pakamwa.+Akuimba mluzu ndi kukukukutira mano.+ Iwo akunena kuti: “Ameneyu timumeza.+Ndithu, lero ndi tsiku limene takhala tikuyembekezera.+ Lafikadi! Taliona!”+