Yesaya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nʼchifukwa chake akunyamula zinthu zimene zatsala pa katundu amene anasunga komanso chuma chawo.Iwo akuwoloka chigwa* cha mitengo ya msondodzi.
7 Nʼchifukwa chake akunyamula zinthu zimene zatsala pa katundu amene anasunga komanso chuma chawo.Iwo akuwoloka chigwa* cha mitengo ya msondodzi.