Yesaya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 N’chifukwa chake akumanyamula zinthu zotsala ndi katundu amene anasunga, n’kumapita nazo kuchigwa* cha mitengo ya msondodzi.
7 N’chifukwa chake akumanyamula zinthu zotsala ndi katundu amene anasunga, n’kumapita nazo kuchigwa* cha mitengo ya msondodzi.