Yesaya 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu anga amene abalalitsidwa akhale mʼdziko lako, iwe Mowabu. Iwe ukhale malo awo obisalamo pamene akuthawa wowononga.+ Wopondereza adzafika pamapeto ake,Chiwonongeko chidzatha,Ndipo amene akupondaponda anzawo adzatha padziko lapansi.
4 Anthu anga amene abalalitsidwa akhale mʼdziko lako, iwe Mowabu. Iwe ukhale malo awo obisalamo pamene akuthawa wowononga.+ Wopondereza adzafika pamapeto ake,Chiwonongeko chidzatha,Ndipo amene akupondaponda anzawo adzatha padziko lapansi.