Yesaya 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu anga obalalika akhale ngati alendo mwa iwe Mowabu.+ Iwo abisale mwa iwe pothawa wolanda,+ pakuti wopondereza anthu wafika pamapeto ake. Kulanda kwatha. Opondaponda anzawo atha padziko lapansi.+
4 Anthu anga obalalika akhale ngati alendo mwa iwe Mowabu.+ Iwo abisale mwa iwe pothawa wolanda,+ pakuti wopondereza anthu wafika pamapeto ake. Kulanda kwatha. Opondaponda anzawo atha padziko lapansi.+