1 Samueli 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Davide anachoka kupita ku Mizipe, ku Mowabu ndi kupempha mfumu ya Mowabu+ kuti: “Chonde, lolani kuti bambo ndi mayi anga+ akhale nanu kufikira nditadziwa zimene Mulungu adzandichitira.”
3 Kenako Davide anachoka kupita ku Mizipe, ku Mowabu ndi kupempha mfumu ya Mowabu+ kuti: “Chonde, lolani kuti bambo ndi mayi anga+ akhale nanu kufikira nditadziwa zimene Mulungu adzandichitira.”