Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komanso ndikugula Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira+ libwerere pacholowa chake, kutinso lisafafanizike pakati pa abale ake ndi mumzinda wathu. Inu ndinu mboni+ lero.”

  • Rute 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo akazi okhala naye pafupi+ anatcha mwanayo dzina lakuti Obedi.+ Ndipo iwo anati: “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Obedi ndiye bambo ake a Jese,+ bambo ake a Davide.

  • 1 Samueli 14:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Tsopano Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli+ ndipo anamenya nkhondo ndi adani ake onse om’zungulira. Iye anamenyana ndi Mowabu,+ ana a Amoni,+ Edomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene anali kutembenukira anali kuwalanga.+

  • 1 Samueli 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena