Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 47:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chotero Yosefe anakhazika bambo ake ndi abale akewo ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino koposa a dzikolo ku Ramese,+ monga mmene Farao analamulira.

  • Ekisodo 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+

  • Miyambo 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Bambo wa munthu wolungama ndithu adzasangalala.+ Bambo wobereka mwana wanzeru adzakondwera naye.+

  • Mateyu 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,+ komanso lakuti, Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena