Levitiko 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu amtundu wako.+ Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova. Mateyu 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Lachiwiri lofanana nalo ndi ili, ‘Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’+ Maliko 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Lachiwiri ndi ili, ‘Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’+ Kulibe lamulo lina lalikulu kuposa amenewa.” Luka 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anayankha kuti: “‘Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, mphamvu zako zonse, ndi maganizo ako onse.’+ Komanso, ‘uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’”+
18 “‘Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu amtundu wako.+ Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova.
31 Lachiwiri ndi ili, ‘Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’+ Kulibe lamulo lina lalikulu kuposa amenewa.”
27 Iye anayankha kuti: “‘Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, mphamvu zako zonse, ndi maganizo ako onse.’+ Komanso, ‘uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’”+