Yeremiya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofunkha adzalowa mumzinda uliwonse+ ndipo sipadzapezeka mzinda wopulumuka.+ Zigwa ndi malo athyathyathya adzawonongedwa ndithu, izi ndi zimene Yehova wanena. Yeremiya 48:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “‘Mowabu adzawonongedwa ndipo sadzakhalanso mtundu wa anthu+ chifukwa wadzikweza pamaso pa Yehova.+
8 Wofunkha adzalowa mumzinda uliwonse+ ndipo sipadzapezeka mzinda wopulumuka.+ Zigwa ndi malo athyathyathya adzawonongedwa ndithu, izi ndi zimene Yehova wanena.
42 “‘Mowabu adzawonongedwa ndipo sadzakhalanso mtundu wa anthu+ chifukwa wadzikweza pamaso pa Yehova.+