Yesaya 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ife tamva za kunyada kwa Mowabu, iye ndi wonyada kwambiri.+Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake ndi mkwiyo wake.+Koma zolankhula zake zopanda pake sizidzachitika.
6 Ife tamva za kunyada kwa Mowabu, iye ndi wonyada kwambiri.+Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake ndi mkwiyo wake.+Koma zolankhula zake zopanda pake sizidzachitika.