Yesaya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masana umamanga mpanda bwinobwino kuzungulira munda wakowo,Ndipo mʼmawa umachititsa kuti mbewu yako iphuke.Koma zokolola zake zidzasowa pa tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:11 Yesaya 1, ptsa. 196-197
11 Masana umamanga mpanda bwinobwino kuzungulira munda wakowo,Ndipo mʼmawa umachititsa kuti mbewu yako iphuke.Koma zokolola zake zidzasowa pa tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+