-
Yesaya 17:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Madzulo kudzakhala zoopsa.
Kusanache, adaniwo kudzakhala kulibe.
Izi nʼzimene zidzachitikire anthu amene akutilanda zinthu zathu
Ndipo ndi cholowa cha anthu amene akuba katundu wathu.
-