Yesaya 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Madzulo kudzakhala zoopsa zamwadzidzidzi. Kusanache, zidzachoka.+ Izi n’zimene zidzachitikire anthu otilanda zinthu, ndipo n’zimene zidzagwere anthu oba katundu wathu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:14 Yesaya 1, ptsa. 198-199
14 Madzulo kudzakhala zoopsa zamwadzidzidzi. Kusanache, zidzachoka.+ Izi n’zimene zidzachitikire anthu otilanda zinthu, ndipo n’zimene zidzagwere anthu oba katundu wathu.+