2 Mafumu 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri+ n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+ Salimo 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma anafa ndipo sanapezekenso.+Ndinamufunafuna ndipo sindinamupeze.+
35 Ndiyeno usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri+ n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+