-
Yesaya 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Asodzi adzalira,
Anthu oponya mbedza mumtsinje wa Nailo adzalira,
Ndipo chiwerengero cha anthu amene amaponya maukonde awo mʼmadzi chidzachepa.
-