Yesaya 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Asodzi a nsomba adzalira ndipo onse oponya mbedza mumtsinje wa Nailo adzamva chisoni. Ngakhale oponya maukonde ophera nsomba pamadziwo adzalefuka.+
8 Asodzi a nsomba adzalira ndipo onse oponya mbedza mumtsinje wa Nailo adzamva chisoni. Ngakhale oponya maukonde ophera nsomba pamadziwo adzalefuka.+