-
Yesaya 19:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehova adzadziwika bwino kwa Aiguputo, ndipo Aiguputowo adzamudziwa Yehova pa tsiku limenelo. Iwo adzapereka nsembe ndi mphatso ndipo adzachita lonjezo kwa Yehova nʼkulikwaniritsa.
-