Yesaya 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adzadziwika bwino kwa Aiguputo,+ ndipo Aiguputowo adzamudziwa Yehova m’tsiku limenelo. Iwo adzapereka nsembe ndi mphatso+ ndiponso adzachita lonjezo kwa Yehova n’kulikwaniritsa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:21 Yesaya 1, ptsa. 205-206
21 Yehova adzadziwika bwino kwa Aiguputo,+ ndipo Aiguputowo adzamudziwa Yehova m’tsiku limenelo. Iwo adzapereka nsembe ndi mphatso+ ndiponso adzachita lonjezo kwa Yehova n’kulikwaniritsa.+