Yesaya 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mʼchaka chimene Tatani* anatumizidwa ku Asidodi+ ndi Mfumu Sarigoni ya Asuri, anamenyana ndi mzindawo nʼkuulanda.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:1 Nsanja ya Olonda,5/1/2015, tsa. 92/15/1988, tsa. 25 Yesaya 1, ptsa. 210-211
20 Mʼchaka chimene Tatani* anatumizidwa ku Asidodi+ ndi Mfumu Sarigoni ya Asuri, anamenyana ndi mzindawo nʼkuulanda.+