Yesaya 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’chaka chimene Tatani*+ anapita ku Asidodi,+ atatumidwa ndi Sarigoni mfumu ya Asuri,+ n’kukamenyana ndi mzinda wa Asidodi n’kuulanda,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:1 Nsanja ya Olonda,5/1/2015, tsa. 92/15/1988, tsa. 25 Yesaya 1, ptsa. 210-211
20 M’chaka chimene Tatani*+ anapita ku Asidodi,+ atatumidwa ndi Sarigoni mfumu ya Asuri,+ n’kukamenyana ndi mzinda wa Asidodi n’kuulanda,+