2 Mbiri 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pa zimenezi, Senakeribu+ mfumu ya Asuri ali ku Lakisi+ pamodzi ndi asilikali ake onse,+ anatumiza atumiki ake ku Yerusalemu kwa Hezekiya mfumu ya Yuda ndi kwa anthu onse okhala ku Yudeya ku Yerusalemu. Anawatuma kukanena kuti:
9 Pambuyo pa zimenezi, Senakeribu+ mfumu ya Asuri ali ku Lakisi+ pamodzi ndi asilikali ake onse,+ anatumiza atumiki ake ku Yerusalemu kwa Hezekiya mfumu ya Yuda ndi kwa anthu onse okhala ku Yudeya ku Yerusalemu. Anawatuma kukanena kuti: