Yesaya 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzachita mantha komanso adzachita manyazi ndi Itiyopiya amene ankamudalira ndiponso ndi Iguputo amene ankamunyadira.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:5 Yesaya 1, ptsa. 212-214
5 Iwo adzachita mantha komanso adzachita manyazi ndi Itiyopiya amene ankamudalira ndiponso ndi Iguputo amene ankamunyadira.*