Yesaya 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzachita mantha ndiponso manyazi chifukwa chakuti anali kudalira Itiyopiya+ komanso chifukwa chakuti anali kusirira kukongola kwa Iguputo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:5 Yesaya 1, ptsa. 212-214
5 Iwo adzachita mantha ndiponso manyazi chifukwa chakuti anali kudalira Itiyopiya+ komanso chifukwa chakuti anali kusirira kukongola kwa Iguputo.+