2 Mafumu 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika+ loti munthu ataligwira kuti limuchirikize, lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira. Yesaya 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chitetezo cha Farao chidzakhala chochititsa manyazi kwa amuna inu,+ ndipo kubisala mumthunzi wa Iguputo kudzakhala chinthu chopereka chitonzo.+ Yesaya 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+ Yeremiya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+ Ezekieli 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse okhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ chifukwa chakuti iwo anali ngati bango loyendera la nyumba ya Isiraeli.+
21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika+ loti munthu ataligwira kuti limuchirikize, lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.
3 Chitetezo cha Farao chidzakhala chochititsa manyazi kwa amuna inu,+ ndipo kubisala mumthunzi wa Iguputo kudzakhala chinthu chopereka chitonzo.+
6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+
5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+
6 Anthu onse okhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ chifukwa chakuti iwo anali ngati bango loyendera la nyumba ya Isiraeli.+