2 Mafumu 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika+ loti munthu ataligwira kuti limuchirikize, lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira. Yesaya 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chitetezo cha Farao chidzakhala chochititsa manyazi kwa amuna inu,+ ndipo kubisala mumthunzi wa Iguputo kudzakhala chinthu chopereka chitonzo.+ Yesaya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Aiguputowo ndi anthu ochokera kufumbi.+ Si Mulungu ayi. Mahatchi awo ndi zinyama,+ osati mzimu. Yehova akadzatambasula dzanja lake, amene akupereka thandizo adzapunthwa, ndipo amene akuthandizidwawo adzagwa.+ Onsewo adzatha nthawi imodzi. Yesaya 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+ Ezekieli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Farao sadzamutumizira gulu lalikulu la asilikali ndi khamu la anthu kuti amuthandize pankhondo.+ Sadzamuthandiza mwa kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo ndiponso mpanda womenyerapo nkhondo n’cholinga chakuti aphe anthu ambiri.+
21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika+ loti munthu ataligwira kuti limuchirikize, lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.
3 Chitetezo cha Farao chidzakhala chochititsa manyazi kwa amuna inu,+ ndipo kubisala mumthunzi wa Iguputo kudzakhala chinthu chopereka chitonzo.+
3 Koma Aiguputowo ndi anthu ochokera kufumbi.+ Si Mulungu ayi. Mahatchi awo ndi zinyama,+ osati mzimu. Yehova akadzatambasula dzanja lake, amene akupereka thandizo adzapunthwa, ndipo amene akuthandizidwawo adzagwa.+ Onsewo adzatha nthawi imodzi.
6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+
17 Farao sadzamutumizira gulu lalikulu la asilikali ndi khamu la anthu kuti amuthandize pankhondo.+ Sadzamuthandiza mwa kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo ndiponso mpanda womenyerapo nkhondo n’cholinga chakuti aphe anthu ambiri.+