2 Mafumu 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika+ loti munthu ataligwira kuti limuchirikize, lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira. Yesaya 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aiguputo ndi anthu achabechabe ndipo sadzakuthandizani chilichonse.+ Choncho ndinawatcha kuti, “Rahabi.+ Iwo sadzachita chilichonse.” Yeremiya 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu inu mukauze mfumu ya Yuda imene yakutumani kuno kudzafunsira uthenga wa Mulungu kwa ine+ kuti: “Taonani! Gulu lankhondo la Farao limene likubwera kwa anthu inu kuti likuthandizeni lidzabwerera kwawo ku Iguputo.+
21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika+ loti munthu ataligwira kuti limuchirikize, lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.
7 Aiguputo ndi anthu achabechabe ndipo sadzakuthandizani chilichonse.+ Choncho ndinawatcha kuti, “Rahabi.+ Iwo sadzachita chilichonse.”
7 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu inu mukauze mfumu ya Yuda imene yakutumani kuno kudzafunsira uthenga wa Mulungu kwa ine+ kuti: “Taonani! Gulu lankhondo la Farao limene likubwera kwa anthu inu kuti likuthandizeni lidzabwerera kwawo ku Iguputo.+