Ezekieli 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.*+
6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.*+