-
Yesaya 21:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mlondayo anaona galeta lankhondo lokokedwa ndi mahatchi awiri,
Galeta lankhondo lokokedwa ndi abulu,
Galeta lankhondo lokokedwa ndi ngamila.
Iye ankayangʼanitsitsa mwatcheru kwambiri.
-