-
Yesaya 21:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mlondayo anaona magaleta ankhondo okokedwa ndi mahatchi awiriawiri, magaleta ankhondo okokedwa ndi abulu, ndi magaleta ankhondo okokedwa ndi ngamila. Iye anali kuyang’anitsitsa, ndipo anali tcheru kwambiri.
-