Yesaya 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Khalani chete inu anthu okhala mʼmphepete mwa nyanja. Amalonda a ku Sidoni,+ amene amawoloka nyanja, akulemeretsani. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:2 Yesaya 1, ptsa. 245-246
2 Khalani chete inu anthu okhala mʼmphepete mwa nyanja. Amalonda a ku Sidoni,+ amene amawoloka nyanja, akulemeretsani.