Yesaya 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku limenelo, Turo adzaiwalidwa kwa zaka 70,+ mofanana ndi zaka za moyo wa* mfumu imodzi. Pamapeto pa zaka 70 zimenezo, Turo adzakhala ngati hule wamʼnyimbo yakuti: Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:15 Yesaya 1, ptsa. 253-254
15 Pa tsiku limenelo, Turo adzaiwalidwa kwa zaka 70,+ mofanana ndi zaka za moyo wa* mfumu imodzi. Pamapeto pa zaka 70 zimenezo, Turo adzakhala ngati hule wamʼnyimbo yakuti: