Yesaya 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’tsiku limenelo, Turo adzaiwalidwa kwa zaka 70.+ Zimenezi ndi zaka za ulamuliro wa mfumu imodzi. Pamapeto pa zaka 70 zimenezo, Turo adzakhala ngati hule wa m’nyimbo yakuti: Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:15 Yesaya 1, ptsa. 253-254
15 M’tsiku limenelo, Turo adzaiwalidwa kwa zaka 70.+ Zimenezi ndi zaka za ulamuliro wa mfumu imodzi. Pamapeto pa zaka 70 zimenezo, Turo adzakhala ngati hule wa m’nyimbo yakuti: