Yeremiya 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+ Yeremiya 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako, uzitumize kwa mfumu ya Edomu,+ mfumu ya Mowabu,+ mfumu ya ana a Amoni,+ mfumu ya Turo+ ndi mfumu ya Sidoni.+ Upatsire amithenga amene akubwera ku Yerusalemu kudzaonana ndi Zedekiya mfumu ya Yuda. Yeremiya 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+
11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+
3 Kenako, uzitumize kwa mfumu ya Edomu,+ mfumu ya Mowabu,+ mfumu ya ana a Amoni,+ mfumu ya Turo+ ndi mfumu ya Sidoni.+ Upatsire amithenga amene akubwera ku Yerusalemu kudzaonana ndi Zedekiya mfumu ya Yuda.
6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+